Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

September 12-18

MASALIMO 120-134

September 12-18
  • Nyimbo 33 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Thandizo Langa Licokela kwa Yehova”: (Mph. 10)

    • Sal. 121:1, 2—Popeza Yehova analenga zinthu zonse, tili ndi cifukwa comveka com’khulupilila (w04 12/15-CN, tsa. 12 ndime 3)

    • Sal. 121:3, 4—Yehova amakhala chelu nthawi zonse kuti aone zimene atumiki ake akufunikila (w04 12/15-CN, tsa. 12 ndime 4)

    • Sal. 121:5-8—Yehova ndi Mtetezi wokhulupilika wa anthu ake (w04 12/15-CN, tsa. 13 ndime 5-7)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal. 123:2—Kodi fanizo la “maso a atumiki” lili na mfundo yabwanji? (w06 9/1-CN, tsa. 15 ndime 4)

    • Sal. 133:1-3—Ni phunzilo liti limene tingatengepo pa salimo imeneyi? (w06 9/1-CN, tsa. 16 ndime 3)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal.127:1–129:8

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 114

  • Yehova Wanicitila Zambili: (Mph. 15) Tambitsani vidiyo ya pa jw.org. Yehova Wanicitila Zambili. (Pitani pa ZOKHUDZA IFE > ZIMENE TIMACITA.) Kambilanani mafunso otsatilawa: Kodi Yehova anam’thandiza bwanji Crystal? Nanga zimenezi zinam’limbikitsa bwanji? N’ciani cimene anali kucita akayamba kudziona kuti ni wosafunika? Kodi nkhani ya Crystal yakuthandizani bwanji?

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia Mawu Omaliza ndime 1-13

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 119 na Pemphelo