Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

September 19-25

MASALIMO 135-141

September 19-25
  • Nyimbo 59 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Tinapangidwa Modabwitsa”: (Mph. 10)

    • Sal. 139:14—Tikamaganizila za nchito za Yehova, timayamba kumukonda kwambili n’kukhala ndi mtima woyamikila (w07 6/15-CN, tsa. 21 ndime 1-4)

    • Sal. 139:15, 16—Majini ndi maselo athu amaonetsa mphamvu ndi nzelu za Yehova (w07 6/15-CN, tsa. 22-23 ndime 7-11)

    • Sal. 139:17, 18—Anthu ndi apadela kwambili cifukwa cakuti ali na nzelu zokwanitsa kukamba ndi kuganiza (w07 6/15-CN, tsa. 23 ndime 12-13; w06 9/1-CN, tsa. 16 ndime 8)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal. 136:15—Kodi vesi iyi itithandiza bwanji kumvetsetsa nkhani ya m’buku la Ekisodo? (it-1, tsa. 783 ndime 5)

    • Sal. 141:5—Kodi Mfumu Davide anazindikila ciani? (w15 4/15, tsa. 31 ndime 1)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal.139:1-24

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) wp16. Na5 tsa. 16

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) wp16. Na. 5 tsa. 16—Itanilani mwininyumba kumisonkhano.

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) fg phunzilo 8, ndime 8—Thandizani wophunzila kuti aziseŵenzetsa mfundo zimene waphunzila.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU