Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

September 26–October 2

MASALIMO 142–150

September 26–October 2
  • Nyimbo 134 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Yehova Ndi Wamkulu ndi Woyenela Kutamandidwa Kwambili”: (Mph. 10)

    • Sal. 145:1-9—Ukulu wa Yehova ndi wosasanthulika (w04 1/15-CN, tsa. 10 ndime 3-4; tsa. 11 ndime 7-8; tsa. 14 ndime 20-21; tsa. 15 tsa. 2)

    • Sal. 145:10-13—Okhulupilika a Yehova amam’tamanda (w04 1/15-CN, tsa. 16 ndime 3-6)

    • Sal. 145:14-16—Yehova amacilikiza ndi kusamalila okhulupilika ake (w04 1/15-CN, tsa. 17-18 ndime 10-14)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu (Mph. 8)

    • Sal. 143:8—Kodi vesi imeneyi itithandiza bwanji kulemekeza Mulungu tsiku lililonse? (w10 1/15-CN, tsa. 21 ndime 1-2)

    • Sal. 150:6—Kodi vesi yothela m’buku la Salimo itilimbikitsa kucita ciani? (it-2 448)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 145:1-21

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) 1 Pet. 5:7—Phunzitsani Coonadi.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 37:9-11—Phunzitsani Coonadi.

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) fg phunzilo 9 ndime 3—Thandizani wophunzila kuona mmene angaseŵenzetsele mfundo za m’nkhaniyo.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU