Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu amawaona bwanji anthu amene amamufuna-funa?
Lemba: 1 Pet. 5:6, 7
Ulalo: Kodi Mulungu amacita cidwi na aliyense wa ise kufika pati?
○●○ KUBWELELAKO KOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu amacita cidwi na aliyense wa ise kufika pati?
Lemba: Mat. 10:29-31
Ulalo: Tidziŵa bwanji kuti Mulungu amatimvetsetsa?
○●○ KUBWELELAKO KACIŴILI
Funso: Tidziŵa bwanji kuti Mulungu amatimvetsetsa?
Lemba: Sal. 139:1, 2, 4
Ulalo: Kodi timapindula bwanji cifukwa cakuti Mulungu amatisamalila?