September 10-16
YOHANE 3-4
Nyimbo 57 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yesu Alalikila Mayi Wacisamariya”: (10 min.)
Yoh. 4:6, 7—Ngakhale kuti anali atalema, Yesu anatengelapobe mwayi n’kukambilana na mayi wacisamariya (“atatopa” nwtsty mfundo younikila pa Yoh. 4:6)
Yoh. 4:21-24—Makambilano oceza a Yesu pothela pake anakhala ulaliki kwa anthu ambili
Yoh. 4:39-41—Cifukwa ca khama la Yesu, Asamariya ambili anakhulupilila mwa iye
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yoh. 3:29—Kodi vesiyi itanthauza ciani? (“mnzake wa mkwati” nwtsty mfundo younikila)
Yoh. 4:10—Pamene Yesu anachula za “madzi amoyo,” kodi mwina mzimayi wacisamaliya anaganiza za ciani? Koma kodi Yesu anatanthauzanji? (“madzi amoyo,” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 4:1-15
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.
Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) wp16.2 peji 9 mapa. 1-4—Mutu: Kutanthauzila Lemba la Yohane 4:23.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuyambitsa Makambilano Otsogolela ku Ulaliki”: (15 min.) Kukambilana. Tsilizani mwa kulimbikitsa onse kuti mkati mwa wiki ayeseko kuyambitsa makambilano, olo amodzi cabe. Pa msonkhano wotsatila wa mkati mwa wiki, ofalitsa akafotokoze mmene zinayendela.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 35 mapa. 20-27, na bokosi “Ankabwereza Mfundo Pophunzitsa” pa peji 89
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 35 na Pemphelo