September 3-9
YOHANE 1-2
Nyimbo 13 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yesu Acita Cozizwitsa Cake Coyamba”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Yohane.]
Yoh. 2:1-3—Zinacitika pa phwando la cikwati zikanakhala zocititsa manyazi (w15 6/15 peji 4 pala. 3)
Yoh. 2:4-11—Cozizwitsa cimene Yesu anacita cinalimbikitsa cikhulupililo ca ophunzila ake (jy peji 41 pala. 6)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yoh. 1:1—Yohane sanatanthauze kuti wochedwa “Mawu” anali wolingana na Mulungu Wamphamvuzonse. Tikamba conco pa zifukwa ziti? (“Mau,” “anali ndi,” “Mauyo anali mulungu” nwtsty mfundo zounikila)
Yoh. 1:29—N’cifukwa ciani Yohane M’batizi anachula Yesu kuti “Mwanawankhosa wa Mulungu”? (“Mwanawankhosa wa Mulungu” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 1:1-18
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.
Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs peji 50, Mfundo 2
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (8 min.)
Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya September.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 35 mapa. 12-19
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 121 na Pemphelo