October 25-31
YOSWA 15-17
Nyimbo 146 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tetezani Coloŵa Canu Camtengo Wapatali”: (Mph. 10.)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yos. 17:15, 18—Tidziŵa bwanji kuti ku Isiraeli wakale kunali nkhalango yoŵilila? (w15 7/15 32)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yos. 15:1-12 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Itanilani munthuyo ku misonkhano. (th phunzilo 19)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako, gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 4)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 01 mfundo 6, na mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 9)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Lalikilani Uthenga Wabwino Wakuti Dziko Labwino Lili Pafupi!”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo ya nyimbo yopekedwa koyamba yakuti Dziko Latsopano Likubwelalo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 61
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 34 na Pemphelo