September 13-19
YOSWA 1-2
Nyimbo 97 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mmene Mungakhalile na Moyo Wopambana”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yos. 2:4, 5—N’cifukwa ciani Rahabi anasoceletsa anthu amene mfumu inawatuma kuti akafunefune azondi? (w04 12/1 9 ¶1)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yos. 2:1-16 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Baibo—Yobu 26:7. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela mu vidiyo.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 11)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako, gaŵilani bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuyambitsa phunzilo la Baibo. (th phunzilo 16)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Pitilizani Kuphunzitsa Mphamvu Zanu za Kuzindikila”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti “Khalani ndi Cikumbumtima Cabwino”.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb, phunzilo 55
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 2 na Pemphelo