September 27–October 3
YOSWA 6-7
Nyimbo 144 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pewani Zinthu Zopanda Pake”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yos. 6:20—N’ciani cionetsa kuti mzinda wa Yeriko unawonongedwa m’nthawi yocepa? (w15 11/15 15 ¶2-3)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yos. 6:1-14 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaionetse) (th phunzilo 9)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 01 mfundo 3 (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zimene Gulu Likukwanilitsa (Mph. 5) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya September.
Kusamvela Mwadala Kumabweletsa Mavuto: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti ‘Palibe Ngakhale Mawu Amodzi Omwe Sanakwanilitsidwe—Kambali Kake. Ndiyeno, funsani omvetsela mafunso awa: Ni lamulo losapita m’mbali liti limene Yehova anapeleka ponena za mzinda wa Yeriko? Kodi Akani na banja lake anacita ciani? Nanga n’cifukwa ciani? Kodi tiphunzilapo ciani pa nkhaniyi? Limbikitsani onse kuti akaionelele vidiyo yonse.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 57
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 55 na Pemphelo