October 31–November 6
2 MAFUMU 3-4
Nyimbo 151 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nyamulani Mwana Wanu”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
2 Maf. 4:38—Kodi “ana a aneneli” ayenela kuti anali ndani? (it-2 697 ¶2)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Maf. 3:1-12 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 17)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 20)
Nkhani: (Mph. 5) w13 8/15 28-29—Mutu: Mungatengele Bwanji Citsanzo ca Elisa ca Kudzicepetsa pa Utumiki Wanu? (th phunzilo 15)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Mpaka Pamene Akufa Adzaukitsidwa”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Munthu Amene Timam’konda Akamwalila.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 25
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 139 na Pemphelo