CITANI KHAMA PA ULALIKI
Makambilano Acitsanzo
ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu n’ciyani?
Lemba: Yes. 9:6, 7 kapena Mat. 6:9, 10
Ulalo: Kodi Ufumu wa Mulungu udzacita ciyani?
PEZANI MALEMBAWA M’THUBOKSI YATHU:
ULENDO WOBWELELAKO
Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu udzacita ciyani?
Lemba: Sal. 72:16 kapena Mat. 14:19, 20
Ulalo: Ni liti pamene Ufumu wa Mulungu udzalamulila dziko lapansi?
PEZANI SALIMO 72:16 M’THUBOKSI YATHU: