October 2-8
YOBU 1-3
Nyimbo 141 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pitilizani Kuonetsa Kukula kwa Cikondi Canu pa Yehova”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yobu 1:10—Kodi vesiyi itithandiza bwanji kumvetsa mawu a Yesu a pa Mateyu 27:46? (w21.04 11 ¶9)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 3:1-26 (th phunzilo 12)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu na kumusiyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 9)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. ChuIani na kukambilanako vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 20)
Nkhani: (Mph. 5) w22.01 11-12 ¶11-14—Mutu: Muziphunzitsa Mogwila Mtima Monga Yakobo—Muzikamba Mosapita M’mbali Koma Modzicepetsa. (th phunzilo 18)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
N’nali Kuona Kuti Zonse Nikucita Bwino: (Mph. 10) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Kenako funsani omvela mafunso otsatilawa: N’cifukwa ciyani M’bale Birdwell anali kuona kuti ‘zonse akucita bwino’?
Kodi kuganizila lemba la Mateyu 6:33 kunamusintha bwanji?
N’ciyani cina cimene mwaphunzila pa citsanzo ca banjali?
“Seŵenzetsani Tsamba Loyamba la JW.ORG mu Ulaliki”: (Mph. 5) Kukambilana.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 59 mfundo 6 komanso cidule cake, mafunso obweleza na colinga
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 129 na Pemphelo