October 23-29
YOBU 8-10
Nyimbo 107 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Cikondi ca Mulungu Cosasintha Cimatiteteza ku Mabodza a Satana”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yobu 9:32—Kodi tiyenela kucita ciyani ngati sitikumvetsa mfundo inayake m’Baibo? (w10 10/15 6-7 ¶19-20)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 9:20-35 (th phunzilo 11)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 17)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! komanso kambilanani mwacidule mbali yakuti “Zimene Muyenela Kucita Kuti Mupindule Kwambili na Maphunzilo a Baibo Amenewa.” (th phunzilo 3)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 16 mfundo 6 komanso mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Thandizani Anthu Osapembedza Kudziŵa Mlengi Wawo”: (Mph. 10) Kukambilana na kutamba vidiyo.
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt “Kalata Yocokela ku Bungwe Lolamulila” komanso mutu 1 ¶1-7
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 64 na Pemphelo