October 30–November 5
YOBU 11-12
Nyimbo 87 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Njila Zitatu Zopezela Nzelu na Kupindula Nazo”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yobu 12:11—Kodi mfundo ya pa vesiyi itithandiza bwanji kukulitsa luso la kumvetsela? (w08 8/1 11 ¶5)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 12:1-25 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo na kum’siyila kakhadi kopemphela phunzilo la Baibo. (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano. Kenako, chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 13)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 12 cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga (th phunzilo 19)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Makolo—Thandizani Ana Anu Kupeza Nzelu ya Umulungu”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 1 ¶8-15, bokosi pa tsa. 12
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 3 na Pemphelo