CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Esitere.]
Esitere anali mkazi wokongola kwambili (Esitere 2:7)
Esitere anakhalabe wodzicepetsa ngakhale pamene ena anamuyamikila na kumutamanda mopambanitsa (Esitere 2:9, 15; w17.01 25 ¶11; ia 130 ¶15)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zokamba na zocita zanga zimaonetsa kuti ndine wodzicepetsa?’—w17.01 25 ¶12.