Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

October 14-20

MASALIMO 96-99

October 14-20

Nyimbo 66 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Muzilengeza Uthenga Wabwino”!

(Mph. 10)

Muzilalikila uthenga wabwino (Sal. 96:2; w11-CN 3/1 6 ¶1-2)

Uzani anthu uthenga wabwino wa Tsiku la Ciweluzo (Sal. 96:12, 13; w12 9/1 16 ¶1)

Auzeni colinga ca Yehova codzaza dziko lapansi na anthu amene amatamanda dzina lake (Sal. 99:1-3; w12-CN 9/15 12 ¶18-19)

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 96:1​—Kodi nthawi zambili mawu akuti “nyimbo yatsopano” akagwilitsidwa nchito amaonetsa ciyani? (it-2-E 994)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 98:1–99:9 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kudzipeleka​—Mmene Yesu Anacitila Zimenezi

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 10 mfundo 1-2.

5. Kudzipeleka​—Tengelani Citsanzo ca Yesu

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 9

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 67 na Pemphelo