Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

September 9-15

MASALIMO 82-84

September 9-15

Nyimbo 80 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmodzi wa ana a Kora akuyang’ana cisa ca namzeze mosilila pa bwalo la kacisi

1. Muziyamikila Mwayi wa Utumiki Umene Muli Nawo

(Mph. 10)

Timaukonda kwambili utumiki wathu (Sal. 84:1-3; wp16.6 8 ¶2-3)

Muzisangalala na utumiki umene muli nawo m’malo mongolakalaka umene mulibe (Sal. 84:10; w08-CN 7/15 30 ¶3-4)

Yehova ni wabwino kwa onse amene amam’tumikila mokhulupilika (Sal. 84:11; w20.01 17 ¶12)

Utumiki uliwonse uli na madalitso na zovuta zake. Mukamaganizila kwambili pa madalitso, mudzapeza cimwemwe pocita utumiki uliwonse.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 82:3​—N’cifukwa ciyani kuonetsa cikondi kwa “ana amasiye” mu mpingo n’kofunika? (it-1-E 816)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 82:1–83:18 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Cifundo—Mmene Yesu Anaonetsela Khalidwe Limeneli

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 9 mfundo 1-2.

5. Cifundo—Tengelani Citsanzo ca Yesu

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 57

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 130 na Pemphelo