Onani zimene zilipo

Yehova Amapulumutsa Anthu Ake

Nkhani ya m’Baibo ya pa Ekisodo caputa 3 mpaka 15 ni umboni wamphamvu wakuti Mulungu amene anagaŵa Nyanja Yofiila adzakupulumutsani na imwe ngati mumaonetsa cikhulupililo mwa kupilila.

Yozikidwa pa Ekisodo 3:1-22; 4:1-9; 5:1-9; 6:1-8; 7:1-7; 14:5-10, 13-31; 15:1-21.