Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Limbitsani Cikhulupililo Canu!

Limbitsani Cikhulupililo Canu!

AHEBERI 10:39

M’MAŴA

  • 8:40 Nyimbo Zamalimba

  • 8:50 Nyimbo Na. 119 na Pemphelo

  • 9:00 N’cifukwa Ciani Tiyenela Kulimbitsa Cikhulupililo Cathu Pali Pano?

  • 9:15 Kodi Mukuona “Wosaonekayo”?

  • 9:30 “Munthu Amakhala Ndi Cikhulupililo Cifukwa ca Zimene Wamva”

  • 9:55 Nyimbo Na. 104 na Zilengezo

  • 10:05 “Makhalidwe Amene Mzimu Woyela Umatulutsa Ndiwo, . . . Cikhulupililo”

  • 10:35 Kudzipatulila na Ubatizo

  • 11:05 Nyimbo Na. 50

MASANA

  • 12:20 Nyimbo Zamalimba

  • 12:30 Nyimbo Na. 3

  • 12:35 Zocitika

  • 12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 13:15 Yosiilana: Thandizani Ena Kulimbitsa Cikhulupililo Cawo

    • • Thandizani Mwana Wanu Wacicepele

    • • Thandizani Wophunzila Baibo Wanu

    • • Thandizani Alambili Anzanu

  • 14:00 Nyimbo Na. 38 na Zilengezo

  • 14:10 ‘Yang’anitsitsani Mtumiki Wamkulu ndi Wokwanilitsa Cikhulupililo Cathu’

  • 14:55 Nyimbo Na. 126 na Pemphelo