Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
  1. 1. N’cifukwa ciani tiyenela kulimbitsa cikhulupililo cathu pali pano? (Aheb. 10:39)

  2. 2. Kodi ‘tingamuone’ bwanji Yehova ngakhale kuti ni wosaoneka? (Aheb. 11:27)

  3. 3. N’cifukwa ciani kupenda maulosi a m’Baibo n’kopindulitsa? (Aroma 10:17)

  4. 4. Kodi mzimu woyela ungatithandize bwanji kukhala na cikhulupililo? (Luka 11:13; Agal. 5:22)

  5. 5. Kodi tingaŵathandize bwanji ena kulimbitsa cikhulupililo cawo? (1 Ates. 2:7, 8)

  6. 6. N’cifukwa ciani tiyenela ‘kuyang’anitsitsa Mtumiki Wamkulu ndi Wokwanilitsa cikhulupililo cathu’? (Aheb. 12:2, 3)