Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Onetsani Cikhulupililo!

Onetsani Cikhulupililo!

YOHANE 14:1

M’MAŴA

  • 8:30 Nyimbo Zamalimba

  • 8:40 Nyimbo Na. 118 na Pemphelo

  • 8:50 Onetsani Cikhulupililo!—Motani, Cifukwa Ciani?

  • 9:05 Yosiyilana: Tengelani Citsanzo ca Amene Anaonetsa Cikhulupililo

    • • Isaki na Rabeka

    • • Esitere

    • • Timoteyo

  • 10:05 Nyimbo Na. 60 na Zilengezo

  • 10:15 “Tili ndi Cikhulupililo, Cotelo Tikulankhula”

  • 10:30 Kudzipatulila na Ubatizo

  • 11:00 Nyimbo Na. 52

MASANA

  • 12:10 Nyimbo Zamalimba

  • 12:20 Nyimbo Na. 9 na Pemphelo

  • 12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Onetsani Cikhulupililo mwa Mulungu “Amene Sanganame”

  • 13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 13:30 Nyimbo Na. 54 na Zilengezo

  • 13:40 Yosiyilana: ‘Yendani mwa Cikhulupililo’ Tsiku Lililonse

    • • “Musamade Nkhawa”

    • • “Muzigwilitsa Nchito Bwino Nthawi Yanu”

    • • Pitilizani Kusakhala “Mbali ya Dziko”

  • 14:40 “Yehova Amadziŵa Anthu Ake”

  • 15:15 Nyimbo Na. 7 na Pemphelo