Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
  1. 1. Ngati tionetsa cikhulupililo cathu, kodi padzakhala zotulukapo zotani? (Yohane 3:16)

  2. 2. Kodi tingatengele bwanji citsanzo ca Isaki na Rabeka, Esitere, komanso Timoteyo? (Mlal. 4:11, 12; Sal. 119:46; 2 Tim. 1:5)

  3. 3. N’ciani cingatilimbikitse kuti tipitilizebe kulalikila olo tikumane na zovuta? (2 Akor. 4:13)

  4. 4. Kodi tiyenela kucita ciani kuti ‘tiziyenda mwa cikhulupililo’ tsiku lililonse? (2 Akor. 5:7)

  5. 5. Kodi tiyenela kucita ciani kuti tidziŵike kwa Yehova? (2 Tim. 2:19; Yak. 4:6; 2 Akor. 13:5)