Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mawu kwa Osonkhana

Mawu kwa Osonkhana

UBATIZO Akulu a mpingo wanu anapanga makonzedwe a mmene ubatizo wanu udzacitikila pambuyo pa cigawo ca m’maŵa pa Tsiku Laciŵili.

ZOPELEKA Msonkhano uno ukumasulidwa m’zinenelo zoposa 400. Zopeleka zanu zaufulu zimathandiza pa nchito ya padziko lonse imeneyi. Mungacite copeleka kupitila pa intaneti mwa kupita pa copeleka.pr418.com. Timayamikila kwambili zopeleka zanu zonse. Bungwe Lolamulila limayamikila ngako kuwolowa manja kwanu kocilikiza zinthu za Ufumu.

SUKULU YA ALENGEZI A UFUMU Apainiya a zaka 23 mpaka 65, amene afuna kuwonjezela utumiki wawo, akupemphedwa kuonana na kalembela wa mpingo wawo kuti asaine fomu ya pa intaneti, yofunsila kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu.

Wokonzedwa na Bungwe Lolamulila la Mboni za Yehova

© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania