Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Laciŵili

Tsiku Laciŵili

‘Menyani mwamphamvu nkhondo ya cikhulupililo’​—Yuda 3

M’MAŴA

  • 9:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 9:30 Nyimbo Na. 57 na Pemphelo

  • 9:40 YOSIYILANA: Kumbukilani​—Anthu Opanda Cikhulupililo Angapeze Cikhulupililo!

    • • Anineve (Yona 3:5)

    • • Abale a Yesu Akuthupi (1 Akorinto 15:7)

    • • Anthu Ochuka (Afilipi 3:7, 8)

    • • Anthu Osapembedza (Aroma 10:13-15; 1 Akorinto 9:22)

  • 10:30 Mangani Cikhulupililo mwa Kuseŵenzetsa Buku Lakuti, Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (Yohane 17:3)

  • 10:50 Nyimbo Na. 67 na Zilengezo

  • 11:00 YOSIYILANA: Omenya Nkhondo ya Cikhulupililo Mwacipambano

    • • Aja Amene Mnzawo wa m’Cikwati si Mboni (Afilipi 3:17)

    • • Amene Akuleledwa na Kholo Limodzi (2 Timoteyo 1:5)

    • • Akhristu Amene Sali Pabanja (1 Akorinto 12:25)

  • 11:45 UBATIZO: Pokhala na Cikhulupililo, Tidzapeza Moyo Wosatha! (Mateyu 17:20; Yohane 3:16; Aheberi 11:6)

  • 12:15 Nyimbo Na. 79 na Kupumula

MASANA

  • 13:35 Vidiyo ya Nyimbo

  • 13:45 Nyimbo Na. 24

  • 13:50 YOSIYILANA: Mmene Abale Athu Akuonetsela Cikhulupililo . . .

    • • mu Africa

    • • ku Asia

    • • ku Europe

    • • ku North America

    • • ku Oceania

    • • ku South America

  • 14:15 YOSIYILANA: Loŵani Pakhomo la Zocita Zambili m’Cikhulupililo

    • • Phunzilani Cinenelo Catsopano (1 Akorinto 16:9)

    • • Katumikilenkoni Kumalo Osoŵa (Aheberi 11:8-10)

    • • Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu (1 Akorinto 4:17)

    • • Dzipelekeni Kukathandiza pa Nchito Zomanga za Gulu (Nehemiya 1:2, 3; 2:5)

    • • ‘Ikani Kenakake Pambali’ Kothandizila pa Nchito ya Yehova (1 Akorinto 16:2)

  • 15:15 Nyimbo Na. 84 na Zilengezo

  • 15:20 SEŴELO LA M’BAIBO: Danieli: Citsanzo Cokhala Wokhulupilika kwa Moyo Wonse— Gawo 1(Danieli 1:1–2:49; 4:1-33)

  • 16:20 ‘Menyani Mwamphamvu Nkhondo ya Cikhulupililo’! (Yuda 3; Miyambo 14:15; Aroma 16:17)

  • 16:55 Nyimbo Na. 38 na Pemphelo Lothela