Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Lacitatu

Tsiku Lacitatu

‘Ngati muli ndi cikhulupililo . . . , zidzacitikadi’​—Mateyu 21:21

M’MAŴA

  • 9:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 9:30 Nyimbo Na. 137 na Pemphelo

  • 9:40 YOSIYILANA: Tengelani Citsanzo ca Akazi a Cikhulupililo Colimba!

    • • Sara (Aheberi 11:11, 12)

    • • Rahabi (Aheberi 11:31)

    • • Hana (1 Samueli 1:10, 11)

    • • Kamtsikana Kaciisiraeli Kotengeledwa ku Ukapolo (2 Mafumu 5:1-3)

    • • Mariya Mayi wa Yesu (Luka 1:28-33, 38)

    • • Mayi wa ku Foinike (Mateyu 15:28)

    • • Marita (Yohane 11:21-24)

    • • Zitsanzo Zamakono (Salimo 37:25; 119:97, 98)

  • 11:05 Nyimbo Na. 142 na Zilengezo

  • 11:15 NKHANI YA ANTHU ONSE: “Khulupililani Uthenga Wabwino” (Maliko 1:14, 15; Mateyu 9:35; Luka 8:1)

  • 11:45 Nyimbo Na. 22 na Kupumula

MASANA

  • 13:35 Vidiyo ya Nyimbo

  • 13:45 Nyimbo Na. 126

  • 13:50 SEŴELO LA M’BAIBO: Danieli: Citsanzo Cokhala Wokhulupilika kwa Moyo Wonse— Gawo 2 (Danieli 5:1–6:28; 10:1–12:13)

  • 14:40 Nyimbo Na. 150 na Zilengezo

  • 14:45 Khalani Amphamvu mwa Cikhulupililo Canu! (Danieli 10:18, 19; Aroma 4:18-21)

  • 15:45 Nyimbo Yatsopano na Pemphelo Lothela