Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Banja la Yehova Logwilizana

Banja la Yehova Logwilizana

AEFESO 4:3

M’maŵa

  • 08:30 Nyimbo Zamalimba

  • 08:40 Nyimbo Na. 85 na Pemphelo

  • 08:50 Muziyamikila Malo Anu m’Banja la Yehova

  • 09:05 Yosiyilana: Anapangitsa Ena Kumva Kuti ni Olandilidwa

    • • Elihu

    • • Lidiya

    • • Yesu

  • 10:05 Nyimbo Na. 100 na Zilengezo

  • 10:15 Pitilizani Kuthandiza Ena Kuti Akhale m’Banja la Yehova

  • 10:30 Kudzipatulila Komanso Ubatizo

  • 11:00 Nyimbo Na. 135

Masana

  • 12:10 Nyimbo Zamalimba

  • 12:20 Nyimbo Na. 132 na Pemphelo

  • 12:30 Nkhani ya Anthu Onse: Kodi Banja Lanu ni Malo a Mpumulo Komanso a Mtendele?

  • 13:00 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 13:30 Nyimbo Na. 136 na Zilengezo

  • 13:40 Yosiyilana: Kodi Mungakhale Bwanji Wolimbikitsa Mtendele?

    • • Lankhulani Mawu “Olimbikitsa”

    • • ‘Yendani m’Cikondi’

    • • Kanizani Adani Athu

  • 14:40 ‘Musaleke Kuyamika Mulungu Cifukwa ca’ Banja Lanu Lauzimu

  • 15:15 Nyimbo Na. 107 na Pemphelo