Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Pezani Mayankha pa Mafunso Awa

Pezani Mayankha pa Mafunso Awa
  1. 1. Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikiladi malo athu m’banja la Yehova? (Aef. 4:3)

  2. 2. Kodi tingapangitse bwanji ena kumva kuti ni olandilidwa? Nanga n’cifukwa ciyani tiyenela kucita zimenezo? (Aroma 15:7)

  3. 3. Kodi tingathandize bwanji anthu ambili mmene tingathele kuti abwele m’banja la Yehova? (Aef. 2:17; 6:15)

  4. 4. Kodi tingalimbikitse bwanji mtendele? (Aef. 4:29; 5:1, 2; 6:13)

  5. 5. Kodi tingakulitse bwanji cikondi pa banja lathu lauzimu? (Aef. 1:15, 16)

© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

CA-copgm23-CIN