Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mawu kwa Osonkhana

Mawu kwa Osonkhana

Ubatizo Akulu a mpingo wanu anapanga makonzedwe a mmene ubatizo wanu udzacitikila pambuyo pa cigawo ca m’maŵa pa Tsiku Laciŵili.

Zopeleka Msonkhano uno ukumasulidwa m’zinenelo zoposa 500. Zopeleka zanu zaufulu zimathandiza pa nchito ya padziko lonse imeneyi. Mungacite copeleka kupitila pa intaneti mwa kupita pa donate.pr418.com. Timayamikila kwambili zopeleka zanu zonse. Bungwe Lolamulila limayamikila ngako kuwolowa manja kwanu kocilikiza zinthu za Ufumu.

Wokonzedwa na Bungwe Lolamulila la Mboni za Yehova

© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania