Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Ziŵelengelo Zonse za mu 2022

Ziŵelengelo Zonse za mu 2022
  • Nthambi za Mboni za Yehova: 86

  • Ciŵelengelo ca Maiko Ocitila Lipoti: 239

  • Ciŵelengelo ca Mipingo Yonse: 117,960

  • Opezeka pa Cikumbutso Padziko Lonse: 19,721,672

  • Amene Anadya Ziphiphilitso Padziko Lonse: 21,150

  • Ofalitsa a Onse Amene Anagwila Nchito Yolalikila: 8,699,048

  • Avaleji ya Ofalitsa Amene Anali kulalikila Mwezi Uliwonse: 8,514,983

  • Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kucokela mu 2021: 0.4

  • Onse Amene Anabatizika b: 145,552

  • Avaleji ya Apainiya c Mwezi Uliwonse: 1,465,202

  • Avaleji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 381,310

  • Maola Onse Amene Tinathela mu Utumiki: 1,501,797,703

  • Avaleji ya Maphunzilo a Baibo d Mwezi Uliwonse: 5,666,996

M’caka ca utumiki ca 2022, e Mboni za Yehova zinaseŵenzetsa ndalama zoposa madola 242 miliyoni posamalila apainiya apadela, amishonale komanso oyang’anila madela pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale na alongo okwana 21,629, amene akutumikila m’maofesi a nthambi. Onse amenewa ali m’Gulu la Padziko Lonse la Atumiki Apadela a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.

a Wofalitsa ni munthu amene amalalikila mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziŵe mmene timapezela ciŵelengeloci, onani nkhani yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?” pa jw.org ku Chichewa.

b Kuti mudziŵe zimene mungacite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?” pa jw.org ku Chichewa.

c Mpainiya ni wa Mboni wacitsanzo cabwino amene amadzipeleka kuti azilalikila uthenga wabwino kwa maola ena ake mwezi uliwonse.

d Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani ya pa jw.org yakuti, “Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?

e Caka ca utumiki ca 2022 cinayamba pa September 1, 2021, ndipo cinasila pa August 31, 2022.