Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tsiku Laciŵili

Tsiku Laciŵili

Khalani oleza mtima kwa onse1 Atesalonika 5:14

M’maŵa

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 58 na Pemphelo

  • 8:40 YOSIYILANA: “Timasonyeza Kuti Ndife Atumikia Mulungu . . . Mwa Kukhala Oleza Mtima”

    • • Pamene Tilalikila (Machitidwe 26:29; 2 Akorinto 6:4, 6)

    • • Potsogoza Maphunzilo a Baibo (Yohane 16:12)

    • • Polimbikitsana Wina na Mnzake (1 Atesalonika 5:11)

    • • Mukamatumikila Monga Mkulu (2 Timoteyo 4:2)

  • 9:30 Inu Amene Mwaonetsedwa Kuleza Mtima, Onetsani Kuleza Mtima! (Mateyu 7:1, 2; 18:23-35)

  • 9:50 Nyimbo Na. 138 na Zilengezo

  • 10:00 YOSIYILANA: ‘Moleza Mtima, PitilizaniKulolelana m’Cikondi’

    • • Acibale Amene si Mboni (Akolose 4:6)

    • • Mnzanu wa mu Ukwati (Miyambo 19:11)

    • • Ana Anu (2 Timoteyo 3:14)

    • • Acibale Odwala Kapena Okalamba (Aheberi 13:16)

  • 10:45 UBATIZO: Kuleza Mtima kwa Yehova Ni Cipulumutso Cathu! (2 Petulo 3:13-15)

  • 11:15 Nyimbo Na. 75 na Zilengezo

Masana

  • 12:35 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:45 Nyimbo Na. 106

  • 12:50 Samalani na Mtima Wongofuna KudzisangalatsaNthawi Yomweyo (1 Atesalonika 4:3-5; 1 Yohane 2:17)

  • 13:15 YOSIYILANA: “Woleza Mtima ni WabwinoKuposa Munthu Wodzikuza”

    • • Tengelani Abele, Osati Adamu (Mlaliki 7:8)

    • • Tengelani Yakobo, Osati Esau (Aheberi 12:16)

    • • Tengelani Mose, Osati Kora (Numeri 16:9, 10)

    • • Tengelani Samueli, Osati Sauli (1 Samueli 15:22)

    • • Tengelani Yonatani, Osati Abisalomu (1 Samueli 23:16-18)

  • 14:15 Nyimbo Na. 87 na Zilengezo

  • 14:25 SEŴELO: ‘Lola Yehova AkutsogolelePanjila Yako’—Gawo 1 (Salimo 37:5)

  • 14:55 ‘Pozunzidwa, Timapilila Moleza Mtima’ (1 Akorinto 4:12; Aroma 12:14, 21)

  • 15:30 Nyimbo Na. 79 na Pemphelo Lothela