3-B
Chati: Aneneli ndi Mafumu a Yuda ndi a Isiraeli (Mbali 2)
Mafumu a Ufumu wa Kumwela (Kupitililza)
777 B.C.E.
Yotamu: zaka 16
762
Ahazi: zaka 16
746
Hezekiya: zaka 29
716
Manase: zaka 55
661
Amoni: zaka ziŵili
659
Yosiya: zaka 31
628
Yehoahazi: miyezi itatu
Yehoyakimu: zaka 11
618
Yehoyakini: miyezi itatu ndi masiku 10
617
Zedekiya: miyezi 11
607
Ababulo motsogozedwa ndi Nebukadinezara aononga Yerusalemu ndi kacisi wake. Zedekiya mfumu yomaliza pa mafumu apadziko lapansi a m’banja la Davide acotsedwa pa ufumu
Mafumu a Ufumu wa Kumpoto (Kupitililza)
c. 803 B.C.E.
Zekariya: analamulila miyezi 6 yokha
N’zotheka kuti panthawiyi Zekariya anayamba kulamulila, komabe ufumu wake unazatsimikizilidwe ca m’ma c. 792
c. 791
Salumu: Mwezi umodzi
c. 780
Manehemu: zaka 10
Pekahiya: zaka ziŵili
c. 778
Peka: zaka 20
c. 758
Hoshiya: zaka 9 kucokela mu c. 748
c. 748
Zioneka kuti ulamulilo wa Hoshiya unakhazikika ndipo n’zothekanso kuti anali kulandila thandizo kucokela kwa mfumu ya Asuri Tigilati Pilesere III m’ma c. 748
740
Asuri agonjetsa Samaliya, ayamba kulamulila Aisiraeli; ufumu wa kumpoto wa mafuko 10 a Isiraeli ukutha
-
Mundanda wa Aneneli
-
Yesaya
-
Mika
-
Zefaniya
-
Yeremiya
-
Nahamu
-
Habakuku
-
Danieli
-
Ezekieli
-
Obadiya
-
Hoseya