Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

18-B

Ndalama ndi Muyezo

Ndalama ndi Muyezo

Ndalama ndi Muyezo m’Malemba Aciheberi

Gera (sekeli 1⁄20)

Magalamu 0.57 / Maonsi 0.01835

Magera 10 = Beka 1

Beka

Magalamu 5.7 / Maonsi 0.1835

Mabeka 2 = Sekeli 1

Pimu

Magalamu 7.8 / Maonsi 0.2508

Pimu 1 = Sekeli 2⁄3

Muyezo wa Sekeli

Sekeli

Magalamu 11.4 / Maonsi 0.367

Sekeli 50 = Mina 1

Mina

magalamu 570 / Maonsi 18.35

Mamina 60 = Talente 1

Talente

Makilogalamu 34.2 / Maonsi 1,101

Dariki (Golide wa ku Perisiya)

Magalamu 8.4 / Maonsi 0.27

Ezara 8:27

Ndalama ndi Muyezo m’ma Malemba Acikristu Acigiliki

Leputoni (Mkuwa kapena bronzi yaciyuda)

Makuadirani 1⁄2

Luka 21:2

Makuadirani (Mkuwa kapena bronzi yaciroma)

Maleputa 2

Mateyu 5:26

Asariyoni (Mkuwa kapena bronzi yaciroma ndi zigawo)

Makuadiranti 4

Mateyu 10:29

Dinari (Siliva yaciroma)

Makuadiranti 64

Magalamu 3.85 / Maonsi 0.124

Mateyu 20:10

Malipilo a Tsiku Limodzi (Maola 12)

Dirakima (Siliva yacigiriki)

Magalamu 3.4 / Maonsi 0.109

Luka 15:8

Malipilo a Tsiku Limodzi (Maola 12)

Madirakima (Siliva yacigiriki)

Madirakima 2

Magalamu 6.8 / Maonsi 0.218

Mateyu 17:24

Malipilo a Masiku Aŵili

Matetiradarakima a ku Anteokeya

Matetiradirakima a ku Turo (Masiliva a sekeli a ku Turo)

Matetiradirakima (Siliva yacigiriki; yochedwanso kobidi ya golide kapena siliva)

Madirakima 4

Magalamu 13.6 / Maonsi 0.436

Mateyu 17:27

Malipilo a Masiku anai

Mina

Madalakima 100

Magalamu 340 / Maonsi 10.9

Luka 19:13

= pafupifupi 100 malipilo atsiku limodzi

Talente

Mamina 60

Makilogalamu 20.4 / Maonsi 654

Mateyu 18:24

Chivumbulutso 16:21

= pafupifupi malipilo azaka 19

Paundi (Yaciroma)

Magalamu 327 / Maonsi 11.5

Yohane 12:3

“Nado weniweni, wokwana magalamu 327”