Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

4-B

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Ciyambi ca Utumiki wa Yesu

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Ciyambi ca Utumiki wa Yesu

NTHAWI

MALO

COCITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

Ca kumapeto kwa 29

Mtsinje wa Yorodano, mwina pafupi ndi kapena kuoloka Yorodano

Yesu abatizika ndi kudzozedwa; Yehova amulengeza kuti ndi Mwana wake ndi kumuvomeleza

3:13-17

1:9-11

3:21-38

1:32-34

Cipululu ca ku Yudeya

Ayesedwa ndi Mdyelekezi

4:1-11

1:12, 13

4:1-13

 

Betaniya kutsidya la Yorodano

Yohane M’batizi azindikila Yesu kuti ndi Mwanawankhosa wa Mulungu; ophunzila oyambilila akhala ndi Yesu

     

1:15, 29-51

Kana wa ku Galileya; Kaperenao

Cozizwitsa coyamba pacikwati, asandutsa madzi kukhala vinyo; acezela Kaperenao

     

2:1-12

30, Pasika

Yerusalemu

Ayeletsa kacisi

     

2:13-25

Akamba ndi Nekodemo

     

3:1-21

Yudeya; Ainoni

Apita kudela la ku Yudeya, ophunzila ake abatizika; ulaliki womaliza wa Yohane wonena za Yesu

     

3:22-36

Tiberiyo; Yudeya

Yohane aikidwa m’ndende; Yesu apita ku Galileya

4:12; 14:3-5

6:17-20

3:19, 20

4:1-3

Sukari, wa ku Samariya

Paulendo wa ku Galileya, aphunzitsa Asamariya

     

4:4-43

Cipululu ca Yudeya