Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

3-A

Chati: Aneneli ndi Mafumu a Yuda ndi a Isiraeli (Mbali 1)

Chati: Aneneli ndi Mafumu a Yuda ndi a Isiraeli (Mbali 1)

Mafumu a Kumwela a Ufumu wa Yuda wa Mafuko Aŵili

997

Rehobowamu: zaka 17

980

Abiya (Abiyamu): zaka 3

978

Asa: zaka 41

937

Yehosafati: zaka 25

913

Yehoramu: zaka 8

c. 906

Ahaziya: caka cimodzi

c. 905

Mfumukazi Ataliya: zaka 6

898

Yehoasi: zaka 40

858

Amaziya: zaka 29

829

Uziya (Azariya): zaka 52

Mafumu a Kumpoto a Ufumu wa Isiraeli wa Mafuko Khumi

997

Yerobowamu: zaka 22

c. 976

Nadabu: zaka ziŵili

c. 975

Basha: zaka 24

c. 952

Ela: zaka ziŵili

Zimiri: masiku 7 (c. 951)

c. 947

Omuri ndi Tibini: zaka zinai

Omuri (yekha): zaka 8

c. 940

Ahabu: zaka 22

c. 920

Ahaziya: zaka ziŵili

c. 917

Yehoramu: zaka 12

c. 905

Yehu: zaka 28

876

Yehoahazi: zaka 14

c. 862

Yehoahazi ndi Yehoasi: zaka zitatu

c. 859

Yehoasi (yekha): zaka 16

c. 844

Yerobowamu Waciŵili: zaka 41

  • Mndandanda wa Aneneli

  • Yehu

  • Eliya

  • Elisa

  • Yona

  • Amosi