Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

12

Kacisi Amene Solomo Anamanga

Kacisi Amene Solomo Anamanga
  1. Maonekedwe a Kacisi

  2. 1 Malo Oyela Koposa (1 Maf. 6:16, 20)

  3. 2 Malo Oyela (2 Mbiri 5:9)

  4. 3 Zipinda Zakudenga (1 Mbiri 28:11)

  5. 4 Zipinda za Mbali (1 Maf. 6:5, 6, 10)

  6. 5 Yakini (1 Maf. 7:21; 2 Mbiri 3:17)

  7. 6 Boazi (1 Maf. 7:21; 2 Mbiri 3:17)

  8. 7 Khonde (1 Maf. 6:3; 2 Mbiri 3:4) (Utali wake wosatsimikizika)

  9. 8 Guwa la Nsembe la Mkuwa (2 Mbiri 4:1)

  10. 9 Nsanja Yamkuwa (2 Mbiri 6:13)

  11. 10 Bwalo Lamkati (1 Maf. 6:36)

  12. 11 Tanki Yamkuwa (1 Maf. 7:23)

  13. 12 Zotengela (1 Maf. 7:27)

  14. 13 Khomo la Mbali (1 Maf. 6:8)

  15. 14 Zipinda Zodyela (1 Mbiri 28:12)