Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

18-A

Malonda ndi Citukuko

Malonda ndi Citukuko
  • Muyezo wa Zinthu Zamadzi

  • Kori (Mitsuko 10 / Mahini 60)

    Malita 220 / Magaloni 58.1

  • Mitsuko (6 yahini)

    Malita 22 / Magaloni 5.81

  • Hini (Zikhatho 12)

    Malita 3.67 / Mapainti 7.75

  • Cikhato (hini 1⁄12)

    Malita 0.31 / Mapainti 0.66

  • Muyezo wa Zinthu Zimene si Zamadzi

  • Omeri (Kori 1 / Maefa 10)

    Malita 220 / Makwati 200

  • Efa (Maseya 3 / Mahomeri 10)

    Malita 22 / Makwati 20

  • Seya (Maomeri 31⁄3)

    Malita 7.33 / Makwati 6.66

  • Omeri (Mtsuko 14⁄5)

    Malita 2.2 / Makwati 2

  • Mtsuko

    Malita 1.22 / Makwati 1.11

  • Makwati

    Malita 1.08 / Makwati 0.98

  • Miyezo ya Mtunda

  • Bango lalitali (Mikono yaitali 6)

    Mamita 3.11 / Mapazi 10.2

  • Bango (Mikono 6)

    Mamita 2.67 / Mapazi 8.75

  • Kuzama

    Mamita 1.8 / Mapazi 6

  • Mkono wautali (M’lifupi la dzanja 7)

    Masentimita 51.8 / Maichesi 20.4.

  • Mkono (ukulu wa dzanja 2 / M’lifupi la dzanja 6)

    Masentimita 44.5 / Maichesi 17.5.

  • Mkono waufupi

    Masentimita 38 / Maichesi 15.

  • Bwalo limodzi la maseŵela la Ciroma

    Mailo ya Ciroma 1⁄8= Mamita 185 / Mapazi 606.95

  1. 1 M’lifupi la cala (m’lifupi la dzanja 1⁄4)

    Masentimita 1.85 / Maichesi 0.73.

  2. 2 M’lifupi la dzanja (M’lifupi la cala 4)

    Masentimita 7.4 / Maichesi 2.9.

  3. 3 Ukulu wa dzanja (M’lifupi la dzanja 3)

    Masentimita 22.2 / Maichesi 8.75.