Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

4-H

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko—Utumiki Womaliza wa Yesu m’Yerusalemu (Mbali 2)

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko—Utumiki Womaliza wa Yesu m’Yerusalemu (Mbali 2)

NTHAWI

MALO

COCITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

Nisani 14

Yerusalemu

Yesu azindikila Yudasi kukhala wom’peleka ndipo amuuza kuti acoke

26:21-25

14:18-21

22:21-23

13:21-30

Akhazikitsa M’gonelo wa Cakudya ca Ambuye (1 Akor. 11:23-25)

26:26-29

14:22-25

22:19, 20, 24-30

 

Anenelatu za kukanidwa ndi Petulo ndi za kuthawa kwa atumwi

26:31-35

14:27-31

22:31-38

13:31-38

Alonjeza mthandizi; fanizo la mpesa weniweni; apeleka lamulo lokondana; pemphelo lomaliza ndi atumwi

     

14:1–17:26

Getsemane

Nkhawa yaikulu m’munda; Kupelekedwa kwa Yesu ndi kumangidwa

26:30, 36-56

14:26, 32-52

22:39-53

18:1-12

Yerusalemu

Afunsidwa ndi Anasi; ayesedwa ndi Kayafa, Sanihedrini; Petulo am’kana

26:57–27:1

14:53–15:1

22:54-71

18:13-27

Yudasi wom’peleka adzimangilila yekha (Mac. 1:18, 19)

27:3-10

     

Aonekela kwa Pilato, ndiyeno kwa Herode, ndipo am’bwezanso kwa Pilato

27:2, 11-14

15:1-5

23:1-12

18:28-38

Pilato ayesa kum’masula koma Ayuda apempha kuti amasule Baraba; amupha pamtengo wonzunzilapo

27:15-30

15:6-19

23:13-25

18:39–19:16

(c. 3:00 masana., Cisanu)

Gologota

Akufa pamtengo wonzunzilapo

27:31-56

15:20-41

23:26-49

19:16-30

Yerusalemu

Acotsa mtembo pamtengo ndi kuika m’manda

27:57-61

15:42-47

23:50-56

19:31-42

Nisani 15

Yerusalemu

Ansembe ndi Afalisi aika asilikali olondela manda ndi kutsekapo

27:62-66

     

Nisani 16

Yerusalemu ndi madela apafupi; Emau

Yesu aukitsidwa; aonekela nthawi zisanu kwa ophunzila ake

28:1-15

16:1-8

24:1-49

20:1-25

Pambuyo pa Nisani 16

Yerusalemu; Galileya

Aonekelanso nthawi zambili kwa ophunzila (1 Akor. 15:5-7; Mac. 1:3-8); apeleka malangizo; awatuma kuti akapenge ophunzila

28:16-20

   

20:26–21:25

Iyara 25

Phili la Maolivi, pafupi ndi Betaniya

Pambuyo pa masiku 40 ataukitsidwa Yesu akwela kumwamba (Mac. 1:9-12)

   

24:50-53