Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

16-B

Mlungu Womaliza wa Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Mbali 2)

Mlungu Womaliza wa Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Mbali 2)

Nisani 12

KULOŴA KWA DZUŴA (Masiku Aciyuda anali kuyamba ndi kutha poloŵa dzuŵa)

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Tsiku laphee ndi ophunzila ake

  • Yudasi akonza ciwembu com’peleka

KULOŴA KWA DZUŴA

Nisani 13

KULOŴA KWA DZUŴA

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Petulo ndi Yohane akonzekela Pasika

  • Yesu ndi atumwi ena afika madzulo

KULOŴA KWA DZUŴA

Nisani 14

KULOŴA KWA DZUŴA

  • Akudya Pasika ndi atumwi

  • Asambitsa mapazi a atumwi

  • Auza Yudasi kuti acoke

  • Ayambitsa mwambo wa Cakudya Camadzulo ca Ambuye

  • Apelekedwa ndi kumangidwa m’munda wa Getsemani

  • Atumwi athaŵa

  • Azengedwa mlandu ndi Khoti Lalikulu kunyumba kwa Kayafa

  • Petulo akana Yesu

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Aonekelanso pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda

  • Apita naye kwa Pilato, ndiyeno kwa Herode, am’bwezanso kwa Pilato

  • Aweluzidwa ndipo aphedwe kumalo ochedwa Gologota

  • Akufa masana ca m’ma 3 koloko

  • Acotsa mtembo ndi kuuika m’manda

KULOŴA KWA DZUŴA

Nisani 15 (Sabata)

KULOŴA KWA DZUŴA

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Pilato alamula kuti aike asilikali pa manda a Yesu

KULOŴA KWA DZUŴA

Nisani 16

KULOŴA KWA DZUŴA

  • Agulilapo zonukhilitsa manda zina

KUTULUKA KWA DZUŴA

  • Aukitsidwa

  • Aonekela kwa ophunzila ake

KULOŴA KWA DZUŴA