Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

4-D

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Utumiki Waukulu wa Yesu m’Galileya (Mbali 2)

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Utumiki Waukulu wa Yesu m’Galileya (Mbali 2)

NTHAWI

MALO

COCITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

31 kapena 32

Kaperenao

Yesu apeleka mafanizo a Ufumu

13:1-53

4:1-34

8:4-18

 

Nyanja ya Galileya

Atontholetsa cimphepo camphamvu ali m’ngalawa

8:18, 23-27

4:35-41

8:22-25

 

Dela la Gadara

Athamangitsila ziŵanda m’nkhumba

8:28-34

5:1-20

8:26-39

 

Mwina ku Kaperenao

Acilitsa mai wodwala nthenda yotaya magazi; aukitsa mwana wa Yairo

9:18-26

5:21-43

8:40-56

 

Kaperenao (?)

Acilitsa wakhungu ndi wosalankhula

9:27-34

     

Nazareti

Am’kananso ku dela la kwao

13:54-58

6:1-5

   

Galileya

Ulendo wacitatu wa ku Galileya; afutukula nchito mwa kutuma atumwi

9:35–11:1

6:6-13

9:1-6

 

Tiberiyo

Herode adula mutu Yohane; Herode athedwa nzelu ndi Yesu

14:1-12

6:14-29

9:7-9

 

32, pafupi ndi Pasika (Yoh 6:4)

Kaperenao (?); NE pafupi ndi Nyanja ya Galileya

Atumwi abwele kucoka paulendo wolalikila; Yesu adyetsa amuna 5,000

14:13-21

6:30-44

9:10-17

6:1-13

NE pafupi ndi Nyanja ya Galileya; Genesarete

Anthu ayesa kulonga Yesu Ufumu; ayenda panyanja; acilitsa ambili

14:22-36

6:45-56

 

6:14-21

Kaperenao

Akuti ndiye “cakudya copatsa moyo”; ambili akhumudwa ndi kumusiya

     

6:22-71

32, pambuyo pa Pasika

Mwina ku Kaperenao

Avumbula miyambo ya anthu

15:1-20

7:1-23

 

7:1

Foinike; Dekapole

Acilitsa mwana wamkazi wacisurofoinike; adyetsa amuna 4,000

15:21-38

7:24–8:9

   

Magadani

Sanapeleke cizindikilo ciliconse kupatulapo ca Yona

15:39–16:4

8:10-12