Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

4-C

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Utumiki Waukulu wa Yesu m’Galileya (Mbali 1)

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Utumiki Waukulu wa Yesu m’Galileya (Mbali 1)

NTHAWI

MALO

COCITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

30

Galileya

Coyamba Yesu alengeza kuti “Ufumu wakumwamba wayandikila”

4:17

1:14, 15

4:14, 15

4:44, 45

Kana; Nazareti; Kaperenao

Acilitsa mwana wa mkulu wa boma; aŵelenga mpukutu wa Yesaya; akanidwa; apita ku Kaperenao

4:13-16

 

4:16-31

4:46-54

Nyanja ya Galileya, pafupi ndi Kaperenao

Aitana ophunzila anai: Simoni ndi Andireya, Yakobo ndi Yohane

4:18-22

1:16-20

5:1-11

 

Kaperenao

Acilitsa apongozi a Simoni ndi ena

8:14-17

1:21-34

4:31-41

 

Galileya

Ulendo woyamba wa ku Galileya ndi ophunzila ake anai

4:23-25

1:35-39

4:42, 43

 

Acilitsa wakhate; khamu la anthu limutsatila

8:1-4

1:40-45

5:12-16

 

Kaperenao

Acilitsa wopuwala

9:1-8

2:1-12

5:17-26

 

Aitana Mateyu; akudya ndi osonkhetsa msonkho; funso la kusala kudya

9:9-17

2:13-22

5:27-39

 

Yudeya

Alalikila m’sunagoge

   

31, Pasika

Yerusalemu

Acilitsa mwamuna wodwala ku Betesida; Ayuda afuna kumupha

     

5:1-47

Abwelako ku Yerusalemu (?)

Ophunzila ake abudula ngala za tiligu pa Sabata; Yesu “Mbuye wa Sabata”

12:1-8

2:23-28

6:1-5

 

Galileya; Nyanja ya Galileya

Acilitsa wopuwala dzanja pa Sabata; khamu limutsatila; Acilitsa ambili

12:9-21

3:1-12

6:6-11

 

Phili pafupi ndi Kaperenao

Asankha atumwi 12

 

3:13-19

6:12-16

 

Pafupi ndi Kaperenao

Ulaliki wa paphili

5:1–7:29

 

6:17-49

 

Kaperenao

Acilitsa wanchito wa kapitawo wa asilikali

8:5-13

 

7:1-10

 

Naini

Aukitsa mwana wa mkazi wamasiye

   

7:11-17

 

Tiberiyo; Galileya (Naini kapena capafupi)

Yohane aikidwa m’ndende atumiza ophunzila ake kwa Yesu; ayamikila Yohane

11:2-19

 

7:18-35

 

Galileya (Naini kapena capafupi)

Mai wocimwa athila mafuta kumapazi ake; fanizo la nkhongole

   

7:36-50

 

Galileya Ulendo waciŵili wokalalikila, ndi ophunzila 12

   

8:1-3

 

Atulutsa ziŵanda; cimo losakhululukidwa

12:22-37

3:19-30

   

Sanapeleke cizindikilo koma ca Yona

12:38-45

     

Amai ake ndi abale ake afika; anena kuti ophunzila ake ndiwo abale ake

12:46-50

3:31-35

8:19-21