4-F
Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko—Utumiki wa Yesu Wakumapeto Kum’maŵa kwa Yorodano
NTHAWI |
MALO |
COCITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
32, Pambuyo pa Cikondwelelo Copeleka Kacisi |
Betaniya kutsidya la Yorodano |
Apita kumene Yohane anali kubatiza; ambili akhulupilila Yesu |
10:40-42 |
|||
Pereya |
Aphunzitsa mizinda ndi m’midzi, ulendo wa kufupi ndi Yerusalemu |
13:22 |
||||
Awalimbikitsa kuloŵa pa khomo lopapatiza; amvela cisoni Yerusalemu |
13:23-35 |
|||||
Mwina ku Pereya |
Aphunzitsa kudzicepetsa; mafanizo: malo olemekezeka kwambili ndi alendo amene anapeleka zifukwa zokanila |
14:1-24 |
||||
Kuwelengela mtengo wokhala wophunzila |
14:25-35 |
|||||
Mafanizo: nkhosa yotaika, ndalama yotaika, mwana woloŵelela |
15:1-32 |
|||||
Mafanizo: mtumiki wosakhulupilika, munthu wacuma ndi Lazaro |
16:1-31 |
|||||
Aphunzitsa za kukhumudwitsa, kukhululukila, ndi cikhulupililo |
17:1-10 |
|||||
Betaniya |
Imfa ya Lazaro ndi kuukitsidwa kwake |
11:1-46 |
||||
Yerusalemu; Efuraimu |
Akonza ciwembu copha Yesu; acoka |
11:47-54 |
||||
Samariya; Galileya |
Acilitsa akhate 10; awauza mmene Ufumu wa Mulungu udzabwelela |
17:11-37 |
||||
Samariya kapena Galileya |
Mafanizo: mkazi wamasiye wolimbikila, Mfalisi ndi wokhometsa msonkho |
18:1-14 |
||||
Pereya |
Aphunzitsa za cikwati ndi kulekana |
|||||
Adalitsa ana |
18:15-17 |
|||||
Funso la munthu wa cuma; fanizo la anganyu m’munda wa mpesa ndi malipilo ofanana |
18:18-30 |
|||||
Mwina ku Pereya |
Kacitatu anenelatu za imfa yake |
18:31-34 |
||||
Pempho lakuti Yakobo ndi Yohane akakhale ndi udindo mu Ufumu |
||||||
Yeriko |
Yeriko Pamene anali kupitamo, anacilitsa amuna aŵili akhungu; acezela Zakeyo; fanizo la ndalama |
18:35–19:28 |