Mfundo za m'Mau a Mulungu
Mfundo za m’Mau a Mulungu
Pezani mayankho mʼBaibulo a mafunso 20 ofunika kwambili.
FUNSO 1
Kodi Mulungu ndani?
Zipembedzo zambili zimaphunzitsa kuti Mulungu ndi wosamvetsetseka kapena mphamvu cabe, koma Baibulo limanena zosiyana ndi zimenezi.
FUNSO 4
Kodi Baibulo ndi Loona pankhani za Sayansi? ‵
Ngati Baibulo ndi locokela kwa Mulungu liyenela kukhala loona pankhani za sayansi.
FUNSO 5
Kodi m’Baibulo Muli uthenga Wotani?
Mavesi okwanila 10 amatipatsa cithunzi cokwanila ca uthenga wa m’Baibulo
Funso 7
Kodi Baibulo linalosela ciani za nthawi yathu ino?
Kodi kuculuka kwa nkhondo, njala, kuphwanya malamulo, kuloŵa pansi kwa makhalidwe abwino kutanthauzanji?
FUNSO 9
N’cifukwa ciani anthu amavutika?
Ngati Mulungu si amene amacititsa mavuto, kodi ndani amawacititsa?
FUNSO 10
N’ciani cimene Baibulo limalonjeza ponena za mtsogolo?WEB:OnPageTitleSentenceCaseN’ciani cimene Baibulo limalonjeza ponena za mtsogolo?
Ciyembekezo ca m’Baibulo ndi cosangalatsa
FUNSO 12
Tingakhale ndi Ciyembekezo Cotani Kaamba ka Anthu Akufa? WEB:OnPageTitleSentenceCaseTingakhale ndi ciyembekezo cotani kaamba ka anthu akufa?
Kodi imfa ndi mapeto a zonse?
FUNSO 13
Kodi Baibulo limakamba ciani za nchito?
Anthu ambili amaona kuti nchito ndi yotopetsa cakuti amangoigwila mokakamizika. Kodi izi ndi zimene Mulungu amafuna?
FUNSO 14
Cuma canu mungacisamalile bwanji??
Mfundo za nzelu za m’Baibulo zingakuthandize kulamulila cuma canu mmalo mwakuti cuma cizikulamulilani.
FUNSO 15
Mungacipeze bwanji cimwemwe?
Baibulo lili ndi mfundo zothandiza kupeza cimwemwe ndi kukhala okhutila.
FUNSO 17
Kodi Baibulo lingathandize bwanji banja lanu?
Phunzilani mmene Banja lanu lingakhalile malo osangalatsa ndi amtendele.
FUNSO 18
Mungayandikile bwanji Mulungu?
N’zotheka inuyo kukhala paubwenzi wabwino kwambili ndi Mulungu.
FUNSO 20
Mungacite ciani kuti mupindule kwambili pamene muŵelenga baibulo?
Mosasamala kanthu ndi mbali iliyonse ya Baibulo imene mungaŵelenge, kupeza mayankho a mafunso anai kungakuthandizeni kupindula kwambili.