Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

FUNSO 4

Kodi Baibulo ndi Loona pankhani za Sayansi? ‵

Kodi Baibulo ndi Loona pankhani za Sayansi? ‵

“Iye anatambasula kumpoto pamwamba pa malo opanda kanthu, ndipo anakoloŵeka dziko lapansi m’malele.”

Yobu 26:7

“Mitsinje yonse imapita kunyanja koma nyanjayo sidzaza. Mitsinjeyo imabwelela kumalo kumene inacokela kuti ikayambilenso kuyenda.”

Mlaliki 1:7

“Pali Winawake amene amakhala pamwamba pa dziko lapansi lozungulila.”

Yesaya 40:22