Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

FUNSO 12

Tingakhale ndi Ciyembekezo Cotani Kaamba ka Anthu Akufa? WEB:OnPageTitleSentenceCaseTingakhale ndi ciyembekezo cotani kaamba ka anthu akufa?

Tingakhale ndi Ciyembekezo Cotani Kaamba ka Anthu Akufa? WEB:OnPageTitleSentenceCaseTingakhale ndi ciyembekezo cotani kaamba ka anthu akufa?

“Musadabwe nazo zimenezi, cifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda acikumbutso adzamva mau ake ndipo adzatuluka.”

Yohane 5:28, 29

“Kudzakhala kuuka kwa olungama ndi osalungama omwe.”

Machitidwe 24:15

“Ndinaona akufa, olemekezeka ndi onyozeka, ataimilila pamaso pa mpando wacifumuwo, ndipo mipukutu inafunyululidwa. Koma mpukutu wina unafunyululidwa, ndiwo mpukutu wa moyo. Ndipo akufa anaweluzidwa malinga ndi zolembedwa m’mipukutuyo, mogwilizana ndi nchito zao. Nyanja inapeleka akufa amene anali mmenemo. Nayonso imfa ndi Manda zinapeleka akufa amene anali mmenemo. Aliyense wa iwo anaweluzidwa malinga ndi nchito zake.”

Chivumbulutso 20:12, 13