Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

FUNSO 19

Kodi mabuku a m’Baibulo ali ndi uthenga wotani?

Kodi mabuku a m’Baibulo ali ndi uthenga wotani?

MALEMBA ACIHEBERI (“CIPANGANO CAKALE”)

PENTATUKE (MABUKU 5):

Genesis, Ekisodo, Levitiko, Numeri, Deuteronomo

Kucokela pacilengedwe mpaka kusankhidwa kwa mtundu wakale wa Isiraeli

MABUKU A MBIRI (MABUKU 12):

Yoswa, Oweluza, Rute

Aisiraeli aloŵa m’Dziko Lolonjezedwa ndi zocitika zina zotsatila

1 ndi 2 Samueli, 1 ndi 2 Mafumu, 1 ndi 2 Mbiri

Mbiri ya mtundu wa Isiraeli mpaka kuonongedwa kwa Yerusalemu

Ezara, Nehemiya, Esitere

Mbili ya Ayuda atabwelako kuukapolo ku Babulo

MABUKU A NDAKATULO (MABUKU 5)

Yobu, Masalimo, Miyambo, Mlaliki, Nyimbo ya Solomo

Mabuku a mau a nzelu ndi nyimbo

MABUKU A ULOSI (MABUKU 17):

Yesaya, Yeremiya, Maliro, Ezekieli, Danieli, Hoseya, Yoweli, Amosi, Obadiya, Yona, Mika, Nahumu, Habakuku, Zefaniya, Hagai, Zekariya, Malaki

Maulosi onena za anthu a Mulungu

MALEMBA ACIGIRIKI ACIKRISTU (“CIPANGANO CATSOPANO”)

MAUTHENGA ABWINO ANAI (MABUKU 4):

Mateyu, Maliko, Luka, Yohane

Mbili ya umoyo wa Yesu ndi utumiki wake

MACITIDWE A ATUMWI (BUKU LIMODZI):

Mbili ya ciyambi ca mpingo wacikristu ndi utumiki waumishonale

MAKALATA (MABUKU 21):

Aroma, 1 ndi 2 Akorinto, Agalatiya, Aefeso, Afilipi, Akolose, 1 ndi 2 Atesalonika

Makalata opita ku mipingo yosiyanasiyana

1 ndi 2 Timoteyo, Tito, Filimoni

Makalata opita kwa Akristu osiyanasiyana

Aheberi, James, 1 ndi 2 Petulo, 1, 2, ndi 3 Yohane, Jude

Makalata cabe opita kwa Akristu

CHIVUMBULUTSO (BUKU LIMODZI):

Masomphenya aulosi osiyanasiyana amene Mtumwi Yohane anaona