Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

FUNSO 20

Mungacite ciani kuti mupindule kwambili pamene muŵelenga baibulo?

Mungacite ciani kuti mupindule kwambili pamene muŵelenga baibulo?

YANKHANI MAFUNSO AWA PAMENE MUŴELENGA BAIBULO LANU:

Kodi zimene ndikuŵelenga zindiuza ciani za Yehova Mulungu?

Kodi mfundo za cigawo ici ca Malemba zimakhudza bwanji uthenga wa m’Baibulo?

Ndingatsatile bwanji zimenezi pa umoyo wanga?

Nanga ndingagwilitsile nchito bwanji mavesi awa kuthandiza ena?

“Mau anu ndi nyale younikila kumapazi anga, ndi kuwala kounikila njila yanga.”

Salimo 119:105