Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela wa 2024-2025 Wokhala na Woimila Nthambi

‘Siticita Manyazi na Uthenga Wabwino’

Ndandanda ya cigawo ca m’mawa na ca masana ca msonkhano wadela wokhala na woimila nthambi.

Pezani Mayankho pa Mafunso Awa

Mafunso amenewa adzayankhidwa msonkhano uli mkati.