Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

‘Siticita Manyazi na Uthenga Wabwino’

‘Siticita Manyazi na Uthenga Wabwino’

AROMA 1:​16

M’maŵa

  • 8:40 Nyimbo Zamalimba

  • 8:50 Nyimbo Na. 67 na Pemphelo

  • 9:00 N’cifukwa Ciyani Siticita Nawo Manyazi Uthenga Wabwino?

  • 9:15 Kukhalila Kumbuyo Uthenga Wabwino

  • 9:30 Khalani “Munthu Wosacita Manyazi ndi Nchito Imene Wagwila”

  • 9:55 Nyimbo Na. 73 na Zilengezo

  • 10:05 Onetsani Mzimu Wamphamvu, Wacikondi, Komanso Woganiza Bwino

  • 10:35 Ubatizo: Pitilizani ‘Kugonjela Uthenga Wabwino’

  • 11:05 Nyimbo Na. 75

Masana

  • 12:20 Nyimbo Zamalimba

  • 12:30 Nyimbo Na. 77

  • 12:35 Zocitika

  • 12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 13:15 Nkhani Yosiyilana: Siticita Nawo Manyazi . . .

    • • Malamulo a Mulungu

    • • Ufumu wa Mulungu

    • • Anthu Oimilako Mulungu

  • 14:00 Nyimbo Na. 40 na Zilengezo

  • 14:10 ‘Dzitamandileni mwa Yehova’

  • 14:55 Nyimbo Na. 7 na Pemphelo