Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Ziŵelengelo Zonse za mu 2020

Ziŵelengelo Zonse za mu 2020
  • Nthambi za Mboni za Yehova: 87

  • Ciŵelengelo ca Maiko ocitila Lipoti: 240

  • Ciŵelengelo ca Mipingo Yonse: 120,387

  • Opezeka pa Cikumbutso Padziko Lonse: 17,844,773

  • Amene Anadya Ziphiphilitso Padziko Lonse: 21,182

  • Ofalitsa Onse Amene Anagwila Nchito Yolalikila *: 8,695,808

  • Avaleji ya Ofalitsa Amene Anali kulalikila Mwezi Uliwonse: 8,424,185

  • Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kucokela mu 2019: -0.6

  • Onse Amene Anabatizika *: 241,994

  • Avaleji ya Apainiya * Mwezi Uliwonse: 1,299,619

  • Avaleji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 338,568

  • Maola Onse Amene Tinathela Mu Utumiki: 1,669,901,531

  • Avaleji ya Maphunzilo a Baibo * Mwezi Uliwonse: 7,705,765

M’caka ca utumiki ca 2020, * Mboni za Yehova zinaseŵenzetsa ndalama zoposa madola 231 miliyoni posamalila apainiya apadela, amishonale komanso oyang’anila madela pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale na alongo okwana 20,994, amene akutumikila m’maofesi a nthambi. Onse amenewa ali m’Gulu la Padziko Lonse la Atumiki Apadela a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.

^ ndime 7 Wofalitsa ni munthu amene amalalikila mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziŵe mmene timapezela ciŵelengelo cimeneci, onani nkhani yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?” pa jw.org ku Chichewa.

^ ndime 10 Kuti mudziŵe zimene mungacite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?” pa jw.org ku Chichewa.

^ ndime 11 Mpainiya ni wa Mboni wacitsanzo cabwino amene amadzipeleka kuti azilalikila uthenga wabwino kwa maola ena ake mwezi uliwonse.

^ ndime 14 Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani ya pa jw.org yakuti, “Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?

^ ndime 15 Caka ca utumiki ca 2020 cinayamba pa September 1, 2019, ndipo cinasila pa August 31, 2020.