Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Ziŵelengelo Zonse za mu 2021

Ziŵelengelo Zonse za mu 2021
  • Nthambi za Mboni za Yehova: 87

  • Ciŵelengelo ca Maiko Ocitila Lipoti: 239

  • Ciŵelengelo ca Mipingo Yonse: 119,297

  • Opezeka pa Cikumbutso Padziko Lonse: 21,367,603

  • Amene Anadya Ziphiphilitso Padziko Lonse: 20,746

  • Ofalitsa a Onse Amene Anagwila Nchito Yolalikila: 8,686,980

  • Avaleji ya Ofalitsa Amene Anali kulalikila Mwezi Uliwonse: 8,480,147

  • Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kucokela mu 2020: 0.7

  • Onse Amene Anabatizika b: 171,393

  • Avaleji ya Apainiya c Mwezi Uliwonse: 1,350,138

  • Avaleji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 398,504

  • Maola Onse Amene Tinathela mu Utumiki: 1,423,039,931

  • Avaleji ya Maphunzilo a Baibo d Mwezi Uliwonse: 5,908,167

M’caka ca utumiki ca 2021, e Mboni za Yehova zinaseŵenzetsa ndalama zoposa madola 229 miliyoni posamalila apainiya apadela, amishonale komanso oyang’anila madela pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale na alongo okwana 20,595, amene akutumikila m’maofesi a nthambi. Onse amenewa ali m’Gulu la Padziko Lonse la Atumiki Apadela a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.

a Wofalitsa ni munthu amene amalalikila mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziŵe mmene timapezela ciŵelengeloci, onani nkhani yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?” pa jw.org ku Chichewa.

b Kuti mudziŵe zimene mungacite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?” pa jw.org ku Chichewa.

c Mpainiya ni wa Mboni wacitsanzo cabwino amene amadzipeleka kuti azilalikila uthenga wabwino kwa maola ena ake mwezi uliwonse.

d Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani ya pa jw.org yakuti, “Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?

e Caka ca utumiki ca 2021 cinayamba pa September 1, 2020, ndipo cinasila pa August 31, 2021.